Aroma 10:20-21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Ndipo Yesaya alimbika mtima ndithu, nati,Ndinapezedwa ndi iwo amene sanandifuna;Ndinaonekera kwa iwo amene sanandifunsa.

21. Koma kwa Israyeli anena, Dzuwa lonse ndinatambalitsira manja anga kwa anthu osamvera ndi okanakana.

Aroma 10