Amosi 9:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Angakhale alowa ndende pamaso pa adani ao, kumeneko ndidzalamulira lupanga, ndipo lidzawapha; ndipo ndidzayang'anitsa maso anga kwa iwowa, kuwacitira coipa, si cokoma ai.

Amosi 9

Amosi 9:1-8