Amosi 8:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ambuye Yehova anandionetsa cotere; ndipo taonani, mtanga wa zipatso zamalimwe.

2. Ndipo anati, Amosi uona ciani? Ndipo ndinati, Mtanga wa zipatso zamalimwe. Nati Yehova kwa ine, Citsiriziro cafikira anthu anga Israyeli, sindidzawalekanso.

3. Koma nyimbo za kukacisi zidzasanduka kubuma tsiku ilo, ati Ambuye Yehova; mitembo idzacuruka; adzaitaya pali ponse padzakhala zii.

Amosi 8