Amosi 3:6-8 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

6. Kodi adzaomba lipenga m'mudzi osanieniemera anthu? Kodi coipa cidzagwera mudzi osacicita Yehova?

7. Pakuti Ambuye Yehova sadzacita kanthu osaulula cinsinsi cace kwa atumiki ace aneneri.

8. Mkango ukabangula, ndani amene saopa? Ambuye Yehova wanena, ndani amene sanenera?

Amosi 3