Amosi 2:15-16 Buku Lopatulika 1992 (BL92) ndi wokoka uta sadzalimbika, ndi waliwiro sadzadzipulumutsa; ngakhale woyenda pa akavalo sadzapulumutsa moyo wace;