Akolose 4:11 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

ndi Yesu, wochedwa Yusto, ndiwo a mdulidwe; iwo okha ndiwo anchito anzanga a mu Ufumu wa Mulungu, ndiwo akundikhalira ine conditonthoza mtima.

Akolose 4

Akolose 4:6-18