Ahebri 13:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92) Cikondi ca pa abale cikhalebe. Musaiwale kucereza alendo; pakuti mwa ici ena anacereza angelo osacidziwa.