Ahebri 12:28-29 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

28. Mwa ici polandira ufumu wosagwedezeka, tikhale naco cisomo, cimene tikatumikire naco Mulungu momkondweretsa, ndi kumcitira ulemu ndi mantha.

29. Pakuti 1 Mulungu wathu ndiye mota wonyeketsa.

Ahebri 12