Ahebri 11:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma cikhulupiriro ndico cikhazikitso ca zinthu zoyembekezeka, ciyesero ca zinthu zosapenyeka.

2. Pakuti momwemo akulu anacitidwa umboru.

Ahebri 11