Agalatiya 4:11-13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

11. Ndiopera inu, kuti kapena odadzibvutitsa ndi inu cabe.

12. Abale, ndikupemphani, khalani monga ine, pakuti inenso ndiri mongainu. Simunandicitira coipa ine;

13. koma mudziwa kuti m'kufoka kwa thupi ndinakulalikirani Uthenga Wabwino poyamba:

Agalatiya 4