Agalatiya 4:1-2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Koma ndinena kuti, pokhala wolowa nyumba ali wakhanda, sasiyana ndi kapolo, angakhale ali mwini zonse;

2. komatu ali wakumvera omsungira ndi adindo, kufikira nthawi yoikika kale ndi atate wace.

Agalatiya 4