Agalatiya 3:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo malonjezano ananenedwa kwa Abrahamu ndi kwa mbeu yace, Sanena, Ndipo kwa zimbeu, ngati kunena zambiri; komatu ngati kunena imodzi, Ndipo kwa mbeu yako, ndiye Kristu.

Agalatiya 3

Agalatiya 3:12-26