2 Timoteo 4:20-22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

20. Erasto anakhalira m'Korinto; koma Trofimo ndamsiya wodwala ku Mileto.

21. 1 Tayesetsa kudza isanadze nyengo yacisanu. Akulankhula iwe Eubulo, ndi Pude, ndi Lino, ndi Klaudiya, ndi abale onse.

22. 2 Ambuye akhale ndi mzimu wako. Cisomo cikhale nanu.

2 Timoteo 4