2 Timoteo 4:2 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

lalikira mau; cita nao pa nthawi yace, popanda nthawi yace; tsutsa, dzudzula, cenjeza, ndi kuleza mtima konse ndi ciphunzitso.

2 Timoteo 4

2 Timoteo 4:1-6