2 Samueli 9:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Davide ananena naye, Usaopa, pakuti zoonadi ndidzakucitira kukoma mtima cifukwa ca Jonatani atate wako; ndi minda yonse ya Sauli ndidzakubwezera, ndipo udzadya pa gome langa cikhalire.

2 Samueli 9

2 Samueli 9:1-13