2 Samueli 19:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Mefiboseti anati kwa mfumu, Lingakhale lonselo alitenge, popeza mbuye wanga mfumu wabwera mumtendere ku nyumba yace.

2 Samueli 19

2 Samueli 19:25-34