2 Samueli 19:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo ngalawa yakuolotsera inaoloka kuti akatenge banja la mfumu ndi kucita comkomera. Ndipo Simeyi mwana wa Gera anagwa pansi pamaso pa mfumu pakuoloka iye pa Yordano.

2 Samueli 19

2 Samueli 19:17-23