2 Samueli 19:16 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Simeyi, mwana wa Gera, Mbenjammi, wa ku Bahurimu, anafulumira natsika pamodzi ndi anthu a Yuda kuti akakomane ndi mfumu Davide.

2 Samueli 19

2 Samueli 19:14-18