2 Samueli 13:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Amnoni anali ndi bwenzi lace, dzina lace ndiye Jonadabu, mwana wa Sineya, mbale wa Davide. Ndipo Jonadabu anali munthu wocenjera ndithu.

2 Samueli 13

2 Samueli 13:1-6