2 Petro 2:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pakuti pakadakhala bwino kwa iwo akadakhala osazindikira njira ya cilungamo, ndi poizindikira, kubwerera kutaya lamulo lopatulika lopatsidwa kwa iwo.

2 Petro 2

2 Petro 2:16-22