2 Mbiri 8:9 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mwa ana a Israyeli Solomo sanawayesa akapolo omgwirira nchito; koma iwowa anali anthu a nkhondo, akazembe ace akuru, ndi akuru a magareta ace, ndi apakavalo ace.

2 Mbiri 8

2 Mbiri 8:1-10