2 Mbiri 6:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

koma akalingirira m'mtima mwao kudziko kumene anawatengera andende, nakatembenuka, nakapembedzera Inu m'dziko la undende wao, ndi kuti, Tacimwa, tacita mphulupulu, tacita coipa;

2 Mbiri 6

2 Mbiri 6:34-39