2 Mbiri 36:15 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Yehova Mulungu wa makolo ao anatumiza kwa iwo, ndi dzanja la mithenga yace, nalawirira mamawa kuituma, cifukwa anamvera cifundo anthu ace, ndi pokhala pace;

2 Mbiri 36

2 Mbiri 36:5-18