2 Mbiri 35:13 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anaoca Paskha pamoto, monga mwa ciweruzo; koma zopatulikazo anaziphika m'miphika, ndi m'mitsuko, ndi m'ziwaya; nazipereka msanga kwa ana onse a anthu.

2 Mbiri 35

2 Mbiri 35:10-19