2 Mbiri 34:25 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

cifukwa anandisiya Ine, nafukizira milungu yina, kuti autse mkwiyo wanga ndi nchito zonse za manja ao; cifukwa cace ukali wanga utsanulidwa pamalo pano wosazimika.

2 Mbiri 34

2 Mbiri 34:19-27