2 Mbiri 33:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pemphero lace lomwe, ndi m'mene Mulungu anapembedzeka naye, ndi chimo lace lonse, ndi kulakwa kwace, ndi apo anamanga misanje, naimika zifanizo ndi mafano osema asanadzicepetse, taonani, zalembedwa m'buku la mau a Hozai.

2 Mbiri 33

2 Mbiri 33:11-25