2 Mbiri 32:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Hezekiya yemweyo anatseka kasupe wa kumtunda wa madzi a Gihoni, nawapambutsa atsikire ku madzulo kwa mudzi wa Davide. Ndipo Hezekiya analemerera nazo nchito zace zonse.

2 Mbiri 32

2 Mbiri 32:25-33