2 Mbiri 28:18 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Afilisti omwe adagwa m'midzi ya kucidikha, ndi ya kumwela kwa Yuda, nalanda Betisemesi, ndi Azaloni, ndi Gederoti, ndi Soko ndi miraga yace, ndi Timna ndi miraga yace; nakhala iwo komweko.

2 Mbiri 28

2 Mbiri 28:8-26