2 Mbiri 25:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Motero anakwera Yoasi mfumu ya Israyeli, ndipo iye ndi Amaziya mfumu ya Yuda anapenyana maso ku Betisemesi, ndiwo wa Yuda.

2 Mbiri 25

2 Mbiri 25:20-26