2 Mbiri 24:6 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mfumu inaitana Yehoyada mkuru wao, niti naye, Unalekeranji kuuza Alevi abwere nao kucokera m'Yuda ndi Yerusalemu msonkho wa Mose mtumiki wa Yehova, ndi wa msonkhano wa Israyeli, ukhale wa cihema ca umboni?

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:1-13