2 Mbiri 24:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mzimu wa Mulungu unabvala Zekariya mwana wa Yehoyada wansembe, naima iye kumtunda kwa anthu, nanena nao, Atero Mulungu, Mulakwiranji malamulo a Yehova kuli kosalemerera nako? Popeza mwasiya Yehova, Iye wasiyanso inu.

2 Mbiri 24

2 Mbiri 24:18-26