2 Mbiri 23:3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo msonkhano wonse unapangana pangano ndi mfumu m'nyumba ya Mulungu. Ndipo ananena nao, Taonani, mwana wa mfumu adzakhala mfumu monga Yehova ananena za ana a Davide.

2 Mbiri 23

2 Mbiri 23:1-11