2 Mbiri 21:4 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Atauka tsono Yehoramu m'ufumu wa atate wace, nadzilimbitsa, anapha ndi lupanga abale ace onse, ndi akalonga ena omwe a Israyeli,

2 Mbiri 21

2 Mbiri 21:1-7