2 Mbiri 20:37 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Pamenepo Eliezeri mwana wa Dodavahu wa Maresa ananenera kumtsutsa Yehosafati, ndi kuti, Popeza waphatikana ndi Ahaziya Yehova wapasula nchito zako. Ndipo zombo zinasweka zosakhoza kumuka ku Tarisi.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:33-37