2 Mbiri 20:1 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo zitatha izi, kunacitika kuti ana a Moabu, ndi ana a Amoni, ndi ena pamodzi ndi Aamoni, anadza kuyambana nkhondo ndi Yehosafati.

2 Mbiri 20

2 Mbiri 20:1-7