2 Mbiri 19:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo tsono, kuopa Yehova kukhale pa inu, musamalire ndi kucita; pakuti palibe cosalungama kwa Yehova Mulungu wathu, kapena kusamalira monga mwa nkhope ya munthu, kapena kulandira mphatso.

2 Mbiri 19

2 Mbiri 19:6-10