2 Mbiri 18:34 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo nkhondo inakula tsiku lija; koma mfumu ya Israyeli inagwirizizil ka m'gareta wace popenyana ndi Aaramu mpaka madzulo, namwalira nthawi yakulowa dzuwa.

2 Mbiri 18

2 Mbiri 18:33-34