2 Mbiri 16:7 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nthawi yomweyi Hanani mlauli anadza kwa Asa mfumu ya Yuda, nanena naye, Popeza mwatama mfumu ya Aramu, osatama Yehova Mulungu wanu, cifukwa cace khamu la nkhondo la mfumu ya Aramu lapulumuka m'dzanja lanu.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:2-10