2 Mbiri 16:12 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Asa atakhala mfumu zaka makumi atatu mpham bu zisanu ndi zitatu, anadwala nthenda ya mapazi, nikuladi nthendayi; koma podwala iye sanafuna Yehova, koma asing'anga.

2 Mbiri 16

2 Mbiri 16:3-14