2 Mbiri 13:21 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma Abiya anakula mphamvu, nadzitengera akazi khumi ndi anai, nabala ana amuna makumi awiri mphambu awiri, ndi ana akazi khumi mphambu asanu ndi mmodzi.

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:13-22