2 Mbiri 13:19 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo Abiya analondola Yerobiamu, namlanda midzi yace, Beteli ndi miraga yace, ndi Yesana ndi miraga yace, ndi Efroni ndi miraga yace.

2 Mbiri 13

2 Mbiri 13:15-22