2 Mbiri 11:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo anacita mwanzeru, nabalalitsa ana ace amuna onse m'maiko onse a Yuda ndi Benjamini, ku midzi yonse yamalinga; nawapatsa cakudya cocuruka, nawafunira akazi ocuruka.

2 Mbiri 11

2 Mbiri 11:18-23