2 Mbiri 10:14 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nalankhula nao monga umo anampangira acinyamata, ndi kuti, Atate wanga analemeretsa goli lanu, koma ine ndidzaonjezerapo; atate wanga anakukwapulani ndi zikoti, koma ine ndidzakukwapulani ndi zinkhanira.

2 Mbiri 10

2 Mbiri 10:7-19