2 Mafumu 9:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo mlonda ali ciriri pacilindiro m'Yezreeli, naona gulu la Yehu lirinkudza, nati, Ndiona gulu. Nati Yoramu, Tenga wapakavalo, numtumize akomane nao, nanene, Mtendere kodi?

2 Mafumu 9

2 Mafumu 9:12-21