2 Mafumu 7:17 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Koma mfumu idayang'anitsa pacipata kazembe amene uja idafotsamira pa dzanja lace; ndipo anthu anampondereza pacipata, nafa iye, monga umo adanenera munthu wa Mulungu, ponena paja anamtsikira mfumu.

2 Mafumu 7

2 Mafumu 7:12-19