2 Mafumu 6:30 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo pakumva mfumu mau a mkaziyo, anang'amba zobvala zace alinkupita nayenda palinga, anthu napenya; ndipo taonani, pali ciguduli m'kati pa thupi lace.

2 Mafumu 6

2 Mafumu 6:22-33