2 Mafumu 6:20 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Ndipo kunali, pakufika ku Samariya, Elisa anati, Yehova, muwakanganulire awa maso kuti aone. Nawakanganulira Yehova maso ao, naona iwo, ndipo tapenyani, ali pakati pa Samariya.

2 Mafumu 6

2 Mafumu 6:13-30