2 Mafumu 6:1-3 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

1. Ndipo ana a aneneri anati kwa Elisa, Taonani tsono, pamalo tikhalapo ife pamaso panu paticepera

2. Mutilole tipite ku Yordano, tikatengeko, ali yense mtengo, tidzimangire malo komweko, tikhalepo, Nati, Mukani.

3. Ndipo wina anati, Mulole mupite nafe anyamata anu. Nati, Ndidzamuka.

2 Mafumu 6