2 Mafumu 5:22 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

Nati, Kuli bwino. Mbuye wanga wandituma, ndi kuti, Taonani, andifikira tsopano apa anyamata awiri a ana a aneneri, ocokera ku mapiri a Efraimu; muwapatse talente wa siliva, ndi zobvala zosintha ziwiri.

2 Mafumu 5

2 Mafumu 5:19-23