2 Mafumu 3:23 Buku Lopatulika 1992 (BL92)

nati, Uja ndi mwazi, atha kuonongana mafumu aja, anakanthana wina ndi mnzace; ndipo tsopano, tiyeni Amoabu inu, tikafunkhe.

2 Mafumu 3

2 Mafumu 3:17-26